Timveni is a media organization focused on children and youth, encompassing both radio and television platforms. This media entity is dedicated to providing a platform for children and young people to advocate for their rights and actively engage with the nation.
Radio iyi mukanangosiya kuulusa dziko lonse mukonze Kaye mavuto omwe alipo zuoneka kut mulibe makina oyenera komanso mulibe ma engineer mungolemba anyamata ootchelera mupira bas kumat ma engineer anu,....manyaka
3
Richard “Richie” kavala05.02.2025
Timveni ikuyenera kuwona ndinso kukonza mbali ya network chifukwa pena pake imasiya kumveka m'madera ambiri.
5
Blethe Theu30.01.2025
Moto unandi
1
Allie Adam Nicholas13.01.2025
Tinven mbambande kuno Cape town
1
Jacob Van j04.01.2025
Simukunveka kuno konzani makina wailesi timaikonda iyi
5
Nelson 28.12.2024
Loud and clear here in LUANAR mother campus
5
Gift Kawere21.12.2024
Arsenal mbambande kuthamanga unga timveni radio
1
Enock BANDA15.12.2024
Timveni pena ikati ibowe aaaa
4
edward london27.11.2024
Timveni ikuvuta masiku ano kumvera online...
5
Raphael eugene Ng'oma09.11.2024
Network yapa internet yikani bwino ma aerial piliz
2
Genesis Bester09.11.2024
Siikuveka kuno ku Blantyre check your server plz
4
Raymond Harrison05.11.2024
Lero radio ikudukaduka kuno ndikudedza
3
Francis Mposa26.10.2024
Crystal clear here in Blantyre
2
Hansen Makwinja22.09.2024
Mmafuna muzikhumudwisatu times zinazake. Mr G. Moyo takonzako eliyo kumeneko simukumvekatu kuno Ku Bangwe takonzeka kale monga ife a #CITY
Connection ndi imene ikuvuta kwanbili koma ikagwira imanveka mbwembwe
1
Amon Malango15.09.2024
1
5
Dennis Nkaonja14.09.2024
Ndine Dennis nkaonja kuno kunathenje police timveni ikuvekabwino anga radio station munakakoloweka kumwezi
5
Tryness Phiri05.09.2024
Nice
5
Adewa Said27.07.2024
Nice
5
Stozen Saduhuh Njovu21.07.2024
Nice
5
John Capital10.07.2024
Tabwelezaniso mutu wo
5
Johnas Chipoka07.07.2024
Loud and Clear kuno ku Nkhatabay
5
Phalyce Kamange28.06.2024
Cheteeee UK pa boma 😂😂😂
5
Aissah Yomex phiri23.06.2024
Timveni on fire all the way from Israel loud and clear
5
Aron Clement Solomon14.05.2024
Radio ilibwino kwambiri. Ine imandisangalatsa ndikamaivela komanso ndimene mumagawila ma program anu. Inu simuli nokha tili nanu limodzi. Koma vuto limene lilipo ndilakuti Kuno ku Lizulu-Ntcheu tikulemphera kuvela ma program anu kusiyana poyamba Loko pa online simukuveka nkomwe chonde takozani makina anuwo tikukusowani ife