Встановіть безкоштовний Online Radio Box на ваш смартфон та слухайте улюблені радіостанції онлайн, де б ви не були!

×
Подобається ? Додайте її до Обраного
×
Подобається ? Залиште свій відгук!
×
×
Підтримуйте Україну. Збережіть мир у світі!

Timveni Online

Лілонгве, 89.6 MHz FM
Рейтинг: 4.3 Оцінок: 105
Timveni is a media organization focused on children and youth, encompassing both radio and television platforms. This media entity is dedicated to providing a platform for children and young people to advocate for their rights and actively engage with the nation.
177 0

Відгуки про Timveni Online

  • 5
    25.08.2025
    Mukumveka akantolora. Gift kawere, from cape town
  • 1
    16.08.2025
    Kuno Ku Durban Chatsworth sikumveka
  • 5
    03.08.2025
    Good
  • 3
    13.07.2025
    Kodi maganizo omwe amapelekedwa pano amagwilitsidwa tchito kapena ayi? Coz anthu ambiri akhala akudandaula kuti radio Madera ambiri simamveka bwino kapenaso kuamveka kumene koma mpaka pano palibe chomwe chikusitha..timveni radio timaikonda anthu ambiri nde pliz chitanipo kanthu kuti zilongosoke
  • 5
    28.06.2025
    I love Timveni Radio
  • 5
    08.06.2025
    ⁰koma alipo akuvera online kapena ndine wamtopola
  • 2
    13.05.2025
    Zayenda bwanj za win big
  • 5
    06.05.2025
    Koma kuno ku port Elizabeth siyikungwira
  • 5
    01.05.2025
    Tikikumvan ndithu from durban it's me king I'm with my wife Anita more fire 🔥 united
  • 5
    16.04.2025
    Enjoying radio Timveni in Lusaka Zambia. Keep it up. we are one.
  • 5
    05.04.2025
    Radio ndiyomweyi palibe kusitha
  • 5
    04.04.2025
    🎉🎉🎉
  • 5
    02.04.2025
    Radio yomvera Mpira ndiyomwei.
  • 5
    29.03.2025
    Nice tune chitimbe ulemu wakk
  • 1
    29.03.2025
    Radio iyi mukanangosiya kuulusa dziko lonse mukonze Kaye mavuto omwe alipo zuoneka kut mulibe makina oyenera komanso mulibe ma engineer mungolemba anyamata ootchelera mupira bas kumat ma engineer anu,....manyaka
  • 3
    05.02.2025
    Timveni ikuyenera kuwona ndinso kukonza mbali ya network chifukwa pena pake imasiya kumveka m'madera ambiri.
  • 5
    30.01.2025
    Moto unandi
  • 1
    13.01.2025
    Tinven mbambande kuno Cape town
  • 1
    04.01.2025
    Simukunveka kuno konzani makina wailesi timaikonda iyi
  • 5
    28.12.2024
    Loud and clear here in LUANAR mother campus

Контакти радіостанції

Адреса: P.O.Box 712,Lilongwe
Телефон: +265992677092
Сайт:
Email: [email protected]
WhatsApp: +265999453453
Facebook: @timveniradio
Twitter: @timvenionline
Instagram: @timvenionline

Area 47,Sector 5
Bwanje Street,House #397
[email protected]
[email protected]

Час в місті Лілонгве: 03:35, 04.29.2026

Встановіть безкоштовний додаток Online Radio Box на ваш смартфон та слухайте улюблені радіостанції онлайн, де б ви не були!