-
Crystal clear here in Blantyre
-
Hansen Makwinja
22.09.2024
Mmafuna muzikhumudwisatu times zinazake. Mr G. Moyo takonzako eliyo kumeneko simukumvekatu kuno Ku Bangwe takonzeka kale monga ife a #CITY
-
Supper from zomba
-
Oscar Wanyøtà (Lil Baby)
18.09.2024
tili limodzi ine OSCAR WANYOTAH
-
Akuwait CK.. Kuno kusikunveka pls takonzani makinawo kumeneko
-
Connection ndi imene ikuvuta kwanbili koma ikagwira imanveka mbwembwe
-
1
-
Dennis Nkaonja
14.09.2024
Ndine Dennis nkaonja kuno kunathenje police timveni ikuvekabwino anga radio station munakakoloweka kumwezi
-
Nice
-
Nice
-
Stozen Saduhuh Njovu
21.07.2024
Nice
-
Tabwelezaniso mutu wo
-
Johnas Chipoka
07.07.2024
Loud and Clear kuno ku Nkhatabay
-
Phalyce Kamange
28.06.2024
Cheteeee UK pa boma 😂😂😂
-
Aissah Yomex phiri
23.06.2024
Timveni on fire all the way from Israel loud and clear
-
Aron Clement Solomon
14.05.2024
Radio ilibwino kwambiri. Ine imandisangalatsa ndikamaivela komanso ndimene mumagawila ma program anu. Inu simuli nokha tili nanu limodzi. Koma vuto limene lilipo ndilakuti Kuno ku Lizulu-Ntcheu tikulemphera kuvela ma program anu kusiyana poyamba Loko pa online simukuveka nkomwe chonde takozani makina anuwo tikukusowani ife
-
Ndiine thoko mwayang'ana from KwaZulu-Natal Ansenal Imenyedw leli
-
Chivwenene Amin
11.04.2024
Ndine Amin Msowoya from karonga boma please ndiyikireni nyimbo iliyose ya Jah Sun or iliyose ya Charles nsako
-
Blessings Jnr Issah
06.04.2024
Wa ain't catching up guys what's wrong
-
Loud and clear here at Nabale
-
Powerful radio station, the sound is just crystal clear
-
Isaac Kamphulu
13.02.2024
Gabe umakwana loude and clear live from Namibia chasaka sagogoda
-
LL, mchesi. Louder and clear
-
Following
-
hadjih jaffali
25.10.2023
nkhotakota bwanji imagwira
-
kenneth mkandawire
29.08.2023
excellent
-
Kasungu ikudukaduka sikuveka bwino
-
Blantyre limbe tikumvera game ya silver ndi bullets koma ikumaduladula kwambiri network
-
Hanif yams kuno ali ndicity tapha ana awa umakwana chitimbe ndinzako
-
Ikujama too much
-
Atickson Semele
10.05.2023
Please ask this Lady yemwe wawelenga nkhani lero za 8 : 00 azikwezako voice coz ukumachita kuposedwa ndi reporter from outside yet iyeyo alimustudio komweko!
-
Frank Kachimanga
02.05.2023
Kuno mayazi sikunveka
-
Why sikumve relo kuno? Please fix the problem
-
Why sikunveka can you fix the problem
-
Vincent Auclair
22.02.2023
Program adapted to the youth. Love it
-
Jamewankhoma Labana
24.09.2022
We need this guys pa timveni Radio
-
Crystal clear; Msundwe Barracks
-
Excellent
-
Love this station
-
Esnelly Ej Moyo
19.05.2022
LUSAKA-ZAMBIA,,,, loud and clear....... munyamata woikonda LIVERPOOL